Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 11:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzakhala, atakulowetsani Yehova Mulungu wanu m'dziko limene mumkako kulilandira, munene mdalitso pa phiri la Gerizimu, ndi temberero pa phiri la Ebala.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 11

Onani Deuteronomo 11:29 nkhani