Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 11:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mukasunga cisungire malamulo awa onse amene ndikuuzani kuwacita; kukonda Yehova Mulungu wanu, kuyenda m'njira zace zonse, ndi kummamatira;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 11

Onani Deuteronomo 11:22 nkhani