Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 10:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku aja Yehova anapatula pfuko la Levi, linyamule likasa la cipangano la Yehova, liimirire pamaso pa Yehova kumtumikira, ndi kudalitsa m'dzina lace kufikira lero lino.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 10

Onani Deuteronomo 10:8 nkhani