Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

bwererani, yendani ulendo wanu ndi kumuka ku mapiri a Aamori, ndi koyandikizana nao, kucidikha, kumapiri, ndi kunsi ndi kumwela, ndi kumphepete kwa nyanja, dziko la Akanani, ndi Lebano, kufikira nyanja yaikuru Firate.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1

Onani Deuteronomo 1:7 nkhani