Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 1:44-46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

44. Ndipo Aamori, akukhala m'mapiri muja, anaturuka kukomana ndi inu, nakupitikitsani, monga zimacita njuci, nakukanthani m'Seiri, kufikira ku Horima.

45. Ndipo munabwerera ndi kulira pamaso pa Yehova; koma Yehova sanamvera mau anu, kapena kukucherani khutu.

46. Potero munakhala m'Kadesi masiku ambiri, monga mwa masiku munakhalako.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1