Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, caka ca makumi anai, mwezi wakhumi ndi umodzi, tsiku loyamba la mweziwo, Mose ananena ndi ana a Israyeli, monga mwa zonse Yehova adamlamulira awauze;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1

Onani Deuteronomo 1:3 nkhani