Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 1:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, Yehova Mulungu wanu wapatsa dzikoli pamaso panu; kwerakoni, landirani, monga Yehova Mulungu wa makolo anu, wanena ndi inu; musamacita mantha, musamatenga nkhawa.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1

Onani Deuteronomo 1:21 nkhani