Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 8:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nayandikira iye poima inepo; atadza iye tsono ndinacita mantha, ndinagwa nkhope pansi; koma anati kwa ine, Zindikira, wobadwa ndi munthu iwe, pakuti masomphenyawo anena za nthawi ya cimariziro.

Werengani mutu wathunthu Danieli 8

Onani Danieli 8:17 nkhani