Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 7:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ufumu, ndi ulamuliro, ndi ukulu wa maufumu, pansi pa thambo lonse, zidzapatsidwa kwa anthu a opatulika a Wam'mwambamwamba; ufumu wace ndiwo ufumu wosatha, ndi maiko onse adzamtumikira ndi kummvera.

Werengani mutu wathunthu Danieli 7

Onani Danieli 7:27 nkhani