Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 7:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinafuna kudziwa coonadi ca cirombo cacinai cija cidasiyana nazo zonsezi, coopsa copambana, mano ace acitsulo, ndi makadabo ace amkuwa, cimene cidalusa, ndi kuphwanya, ndi kupondereza zotsala ndi mapazi ace;

Werengani mutu wathunthu Danieli 7

Onani Danieli 7:19 nkhani