Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 7:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinapenyera cifukwa ca phokoso la mau akuru idanena nyangayi; ndinapenyera mpaka adacipha ciromboci, ndi kuononga mtembo wace, ndi kuupereka utenthedwe ndi moto.

Werengani mutu wathunthu Danieli 7

Onani Danieli 7:11 nkhani