Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 6:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuluwa ndi akalonga anayesa kumtola cifukwa Danieli, kunena za ufumuwo; koma sanakhoza kupeza cifukwa kapena colakwira, popeza anali wokhulupirika; ndipo sanaona cosasamala kapena colakwa ciri conse mwa iye.

Werengani mutu wathunthu Danieli 6

Onani Danieli 6:4 nkhani