Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 6:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anayandikira, nanena pamaso pa mfumu za coletsaco ca mfumu, Kodi simunatsimikiza coletsaco, kuti ali yense akapempha kanthu kwa mulungu ali yense, kapena kwa munthu ali yense, masiku makumi atatu, osati kwa inu nokha, mfumu, adzaponyedwa m'dzenje la mikango? Mfumu niyankha, niti, Coona cinthuci, monga mwa malamulo a Amedi ndi Aperisi amene sasinthika.

Werengani mutu wathunthu Danieli 6

Onani Danieli 6:12 nkhani