Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo podziwa Danieli kuti adatsimikiza colembedwaco, analowa m'nyumba mwace, m'cipinda mwace, cimene mazenera ace anatseguka oloza ku Yerusalemu; ndipo anagwadamaondo ace tsiku limodzi katatu, napemphera, nabvomereza pamaso pa Mulungu wace monga umo amacitira kale lonse.

Werengani mutu wathunthu Danieli 6

Onani Danieli 6:10 nkhani