Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 5:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo cifukwa ca ukulu adampatsawo anthu onse, mitundu yonse ya anthu, a manenedwe onse, ananjenjemera, naopa pamaso pace; amene anafuna kuwapha anawapha; amene anafuna kuwasunga anawasunga amoyo; amene anafuna kuwakweza anawakweza; amene anafuna kuwatsitsa anawatsitsa.

Werengani mutu wathunthu Danieli 5

Onani Danieli 5:19 nkhani