Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nthawi yomweyi nzeru zanga zinandibwerera, ndi cifumu canga ndi kunyezimira kwanga zinandibwerera, kuti uonekenso ulemerero wa ufumu wanga; ndi mandoda anga ndi akuru anga anandifuna; ndipo ndinakhazikika m'ufumu wanga, Iye nandioniezeranso ukulu wocuruka.

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:36 nkhani