Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, mfumu, kupangira kwanga kukomere inu, dulani macimo anu ndi kucita cilungamo, ndi mphulupulu zanu mwa kucitira aumphawi cifundo; kuti kapena nthawi ya mtendere wanu italike.

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:27 nkhani