Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti adzakuingitsani kukucotsani kwa anthu, ndi pokhala panu padzakhala pamodzi ndi nyama za kuthengo; ndipo mudzadya udzu ngati ng'ombe, nimudzakhala wokhathamira ndi mame a kumwamba, nizidzakupitirani nthawi zisanu ndi ziwiri, mpaka mudzadziwa kuti Wam'mwambamwamba alamulira m'ufumu wa anthu, naupereka kwa ali yense Iye afuna mwini.

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:25 nkhani