Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono, kuti mfumu inaona mthenga woyera wotsika kumwamba, ndi kuti, Likhani mtengowo ndi kuuononga, koma siyani citsa cace ndi mizu m'nthaka, comangidwa ndi mkombero wa citsulo ndi mkuwa, mu msipu wa kuthengo, nicikhale cokhathamira ndi mame a kumwamba, ndi gawo lace likhale pamodzi ndi nyama za kuthengo, mpaka zitampitira nthawi zisanu ndi ziwiri;

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:23 nkhani