Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

umene masamba ace anali okoma, ndi zipatso zace zocuruka, ndi m'menemo munali cakudya cofikira onse, umene nyama za kuthengo zinakhala pansi pace, ndi mbalame za m'mlengalenga zinapeza pokhala pao pa nthambi yace;

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:21 nkhani