Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma siyani citsa ndi mizu yace m'nthaka, comangidwa ndi mkombero wa citsulo ndi mkuwa, mu msipu wa kuthengo; ncokhathamira ndi mame a kumwamba, ndi gawo lace likhale pamodzi ndi nyama ziri m'macire a m'dziko.

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:15 nkhani