Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 3:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo akalonga, akazembe, ndi ziwanga, oweruza, akulu osunga cuma, mandoda, ankhoswe, ndi olamulira onse a madera, anasonkhanira kupereka fano adaliimika mfumu Nebukadinezara, naimirira pamaso pa fano adaliimika Nebukadinezara.

Werengani mutu wathunthu Danieli 3

Onani Danieli 3:3 nkhani