Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 3:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukabvomereza tsono, pakumva mau a lipenga, citoliro, zeze, sansi, cisakasa, ndi ngoli, ndi zoyimbitsa ziri zonse, kugwadira ndi kulambira fano ndinalipanga, cabwino; koma mukapanda kulambira, mudzaponyedwa nthawi yomweyi m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto; ndipo mulungu amene adzakulanditsani m'manja mwanga ndani?

Werengani mutu wathunthu Danieli 3

Onani Danieli 3:15 nkhani