Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 2:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo citsulo, dongo, mkuwa, siliva, ndi golidi, zinapereka pamodzi, nizinasanduka ngati mungu wa pa madwale a malimwe; ndi mphepo inaziuluza, osapezekanso malo ao; ndi mwala udagunda fanowo unasanduka phiri lalikuru, nudzaza dziko lonse lapansi.

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:35 nkhani