Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 2:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero Danieli analowa kwa Arioki amene mfumu idamuika aononge eni nzeru a ku Babulo; anamuka, natero naye, Usaononga eni nzeru a ku Babulo, undilowetse kwa mfumu, ndipo ndidzaululira mfumu kumasulirako.

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:24 nkhani