Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 2:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu inauza munthu aitane alembi, ndi openduza, ndi aula, ndi Akasidi, amuululire mfumu maloto ace. Nalowa iwo, naimirira pamaso pa mfumu.

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:2 nkhani