Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 2:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo cinsinsico cinabvumbulutsidwa kwa Danieli m'masomphenya a usiku. Ndipo Danieli analemekeza Mulungu wa Kumwamba.

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:19 nkhani