Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 12:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinamva munthuyo wobvala bafuta wokhala pamwamba pa madzi a mumtsinje, nakweza dzanja lace lamanja ndi lamanzere kumwamba, nalumbira pali Iye wokhala ndi moyo kosatha, kuti zidzacitika nthawi, ndi nthawi zina, ndi nusu; ndipo atatha kumwaza mphamvu ya anthu opatulikawo zidzatha izi zonse.

Werengani mutu wathunthu Danieli 12

Onani Danieli 12:7 nkhani