Wodala iye amene ayembekeza, nafikira ku masiku cikwi cimodzi mphambu mazana atatu kudza makumi atatu ndi asanu.