Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nthawi yomweyi adzauka Mikaeli kalonga wamkuru wakutumikira ana a anthu amtundu wako; ndipo padzakhala nthawi ya masautso, siinakhala yotere kuyambira mtundu wa anthu kufikira nthawi yomwe ija; ndipo nthawi, yomweyo anthu ako adzapulumutsidwa, yense amene ampeza wolembedwa m'buku.

Werengani mutu wathunthu Danieli 12

Onani Danieli 12:1 nkhani