Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 11:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nthawi yotsiriza mfumu ya kumwela idzalimbana naye, ndi mfumu ya kumpoto idzamdzera ngati kabvumvulu, ndi magareta, ndi apakavalo, ndi zombo zambiri; nadzalowa m'maiko, nadzasefukira ndi kupitirira.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:40 nkhani