Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakuuka iye ufumu wace udzatyoledwa, nudzagawikira ku mphepo zinai za mlengalenga; koma sadzaulandira a mbumba yace akudza m'mbuyo, kapena monga mwa ulamuliro wace anacita ufumu nao; pakuti ufumu wace udzazulidwa, ukhale wa ena, si wa aja ai.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:4 nkhani