Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 11:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu idzacita monga mwa cifuniro cace, nidzadzikweza, ndi kudzikuza koposa milungu iri yonse nidzanena zodabwiza pa Mulungu wa milungu, nidzapindula, mpaka udzacitidwa ukaliwo; pakuti cotsimikizika m'mtimaco cidzacitika.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:36 nkhani