Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 11:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzabwerera ku dziko lace ndi cuma cambiri; ndi mtima wace udzatsutsana ndi cipangano copatulika, nadzacita cifuniro cace, ndi kubwerera ku dziko lace.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:28 nkhani