Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 11:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pambuyo pace adzatembenuzira nkhope yace kuzisumbu, nadzalanda zambiri; koma kalonga wina adzaleketsa kunyoza kwace adanyoza nako; inde adzambwezera yekha kunyoza kwace.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:18 nkhani