Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 10:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, wina wakunga ana a anthu anakhudza milomo yanga; pamenepo ndinatsegula pakamwa panga ndi kunena naye woima popenyana nane, Mbuye wanga, cifukwa ca masomphenyawo zowawa zanga zandibwerera, ndipo ndiribenso mphamvu.

Werengani mutu wathunthu Danieli 10

Onani Danieli 10:16 nkhani