Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 1:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mau ali onse anzeru ndi aluntha, amene mfumu inawafunsira, inawapeza akuposa alembi ndi openda onse m'ufumu wace wonse.

Werengani mutu wathunthu Danieli 1

Onani Danieli 1:20 nkhani