Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiye amene amanga zipinda zace zosanja m'mwamba, nakhazika tsindwi lace pa dziko lapansi; Iye amene aitana madzi a m'nyanja, nawatsanulira padziko; dzina lace ndiye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Amosi 9

Onani Amosi 9:6 nkhani