Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 7:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa ine, Amosi, uona ciani? Ndipo ndinati, Cingwe colungamitsira ciriri. Nati Ambuye, Taona, ndidzaika cingwe colungamitsira ciriri pakati pa anthu anga Israyeli, sindidzawalekanso:

Werengani mutu wathunthu Amosi 7

Onani Amosi 7:8 nkhani