Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 7:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace atero Yehova, Mkazi wako adzakhala wadama m'mudzi, ndi ana ako amuna ndi akazi adzagwa ndi lupanga, ndi dziko lako lidzagawanidwa ndi kuyesa cingwe, ndi iwe mwini udzafa m'dziko lodetsedwa; ndipo Israyeli adzatengedwadi ndende kucoka m'dziko lace.

Werengani mutu wathunthu Amosi 7

Onani Amosi 7:17 nkhani