Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 7:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Amaziya wansembe wa ku Beteli anatumiza kwa Yerobiamu mfumu ya Israyeli, ndi kuti, Amosi wapangira inu ciwembu pakati pa nyumba ya Israyeli; dziko silikhoza kulola mau ace onse.

Werengani mutu wathunthu Amosi 7

Onani Amosi 7:10 nkhani