Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mbalewace wa munthu akamnyamula, ndiye womtentha, kuturutsa mafupa m'nyumba, nakati kwa iye ali m'kati mwa nyumbamo, Atsala wina nawe kodi? nakati, lai; pamenepo adzati, Khala cete; pakuti sitingachule dzina la Yehova.

Werengani mutu wathunthu Amosi 6

Onani Amosi 6:10 nkhani