Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 5:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye wakulenga Nsangwe ndi Akamwiniatsatana, nasanduliza mdima wandiweyani ukhale m'mawa, nasanduliza usana ude ngati usiku, wakuitana madzi a m'nyanja, nawatsanulira pa dziko lapansi, dzina lace ndiye Yehova;

Werengani mutu wathunthu Amosi 5

Onani Amosi 5:8 nkhani