Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ine ndakumanani mvula, itatsala miyezi itatu isanafika nyengo yakukolola; ndipo ndinabvumbistira mudzi umodzi mvula, osabvumbitsira mudzi wina; munda wina unabvumbidwa mvula, ndi m'munda mosabvumbidwa mvula munafota.

Werengani mutu wathunthu Amosi 4

Onani Amosi 4:7 nkhani