Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Cifukwa ca zolakwa zitatu za Yuda, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwace; popeza akaniza cilamulo ca Yehova, osasunga malemba ace; ndipo awalakwitsa mabodza ao amene makolo ao anawatsata;

Werengani mutu wathunthu Amosi 2

Onani Amosi 2:4 nkhani