Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 9:12-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Ndipo Mefiboseti anali ndi mwana wamwamuna wamng'ono, dzina lace ndiye Mika. Ndipo onse akukhala m'nyumba ya Ziba anali anyamata a Mefiboseti.

13. Comweco Mefiboseti anakhala ku Yerusalemu, pakuti anadya masiku onse ku gome la mfumu, ndipo anali wopunduka mapazi ace onse awiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 9