Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 9:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uzimlimira munda wace, iwe ndi ana ako ndi anyamata ako; nuzibwera nazo zipatso zace kuti mwana wa mbuye wako akhale ndi zakudya; koma Mefiboseti, mwana wa mbuye wako, adzadya pa gome langa masiku onse. Ndipo Ziba anali nao ana amuna khumi ndi asanu, ndi anyamata makumi awiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 9

Onani 2 Samueli 9:10 nkhani