Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 8:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Davide anaika maboma m'Aramu wa Damasiko, Ndipo Aaramu anasanduka anthu a Davide, nabwera nayo mitulo. Ndipo Yehova anamsunga Davide kuli konse anamukako.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 8

Onani 2 Samueli 8:6 nkhani