Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 8:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaika maboma m'Edomu; m'dziko lonse la Edomu anaika maboma, ndipo Aedomu onse anasanduka anthu a Davide. Ndipo Yehova anasunga Davide kuli konse anamukako.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 8

Onani 2 Samueli 8:14 nkhani