Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 8:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Toi anatumiza mwana wace Joramu kwa mfumu Davide, kuti akamlankhule iye, ndi kumdalitsa, popeza anamenyana ndi Hadadezeri ndi kumkantha; pakuti pakati pa Hadadezeri ndi Toi panali nkhondo. Ndipo Joramu anabwera ndi zotengera zasiliva, ndi zotengera zagolidi, ndi zotengera zamkuwa.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 8

Onani 2 Samueli 8:10 nkhani